This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Inde boma ndichimatchini ndipo chikafuna kuluma sichisewera: Koma kwapano khala ngati manu aguluka. Nalo lalema ndi vuto lakusowa kwa mafuta, mpaka lawuza kampani kuti ziwuyatse ulendo wa kunja zikasake zokha dizilo. Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lati tsopano lipereka chirolezo ku makampani omwe akugwira ntchito zazikulu zachitukuko kuti zipite kuli konse komwe zingathe […]
Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.